4 Mwina Yehova Mulungu amva+ mawu onse a Rabisake, amene mbuye wake mfumu ya Asuri yam’tuma, kuti adzatonze+ nawo Mulungu wamoyo. Ndipo mwina amulanga chifukwa cha mawu amene Yehova Mulungu wanu wamva.+ Inuyo mupereke pemphero+ m’malo mwa otsalira+ amene alipo.’”