2 Mbiri 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma mfumu Hezekiya+ ndi mneneri+ Yesaya+ mwana wa Amozi,+ anali kupempherera nkhani imeneyi+ ndi kufuulira Mulungu kumwamba kuti awapulumutse.+ Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Yakobo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+
20 Koma mfumu Hezekiya+ ndi mneneri+ Yesaya+ mwana wa Amozi,+ anali kupempherera nkhani imeneyi+ ndi kufuulira Mulungu kumwamba kuti awapulumutse.+
16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+