-
2 Mbiri 32:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Tsopano Yehova anatumiza mngelo+ yemwe anapha mwamuna aliyense wamphamvu ndi wolimba mtima,+ komanso mtsogoleri ndi mkulu wa asilikali aliyense mumsasa wa mfumu ya Asuri,+ moti mfumuyo inabwerera kwawo mwamanyazi. Kenako inalowa m’kachisi wa mulungu wake ndipo ili mmenemo, ena mwa ana ake anaipha ndi lupanga.+
-