1 Mafumu 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Maso anu akhale akuyang’ana+ nyumba ino usiku ndi usana. Akhale akuyang’ana malo amene munanena kuti, ‘Dzina langa lidzakhala kumeneko,’+ kuti mumvere pemphero limene mtumiki wanu akupemphera atayang’ana kumalo ano.+ 2 Mafumu 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Yehova anati: “Yuda+ nayenso ndim’chotsa pamaso panga+ monga mmene ndinachotsera Isiraeli,+ ndipo ndithu ndidzakana ngakhale mzinda wa Yerusalemu umene ndinausankha, ndi nyumba imene ndinanena kuti, ‘Dzina langa lizikhala pamenepo.’”+ 2 Mbiri 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndasankha+ ndi kuyeretsa nyumba ino kuti dzina langa+ likhale pamenepa mpaka kalekale,+ ndipo maso anga ndi mtima wanga zidzakhala pamenepa nthawi zonse.+
29 Maso anu akhale akuyang’ana+ nyumba ino usiku ndi usana. Akhale akuyang’ana malo amene munanena kuti, ‘Dzina langa lidzakhala kumeneko,’+ kuti mumvere pemphero limene mtumiki wanu akupemphera atayang’ana kumalo ano.+
27 Koma Yehova anati: “Yuda+ nayenso ndim’chotsa pamaso panga+ monga mmene ndinachotsera Isiraeli,+ ndipo ndithu ndidzakana ngakhale mzinda wa Yerusalemu umene ndinausankha, ndi nyumba imene ndinanena kuti, ‘Dzina langa lizikhala pamenepo.’”+
16 Ndasankha+ ndi kuyeretsa nyumba ino kuti dzina langa+ likhale pamenepa mpaka kalekale,+ ndipo maso anga ndi mtima wanga zidzakhala pamenepa nthawi zonse.+