2 Mbiri 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova anapitiriza kukhala ndi Yehosafati+ chifukwa anayenda m’njira zimene Davide kholo lake+ anayenda kalekale, ndipo sanafunefune Abaala.+ Ezekieli 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Ndiyeno munthu wina wabereka mwana wamwamuna amene amaona machimo onse amene bambo ake amachita. Mwanayo amaona machimowo koma sawachita.+
3 Yehova anapitiriza kukhala ndi Yehosafati+ chifukwa anayenda m’njira zimene Davide kholo lake+ anayenda kalekale, ndipo sanafunefune Abaala.+
14 “‘Ndiyeno munthu wina wabereka mwana wamwamuna amene amaona machimo onse amene bambo ake amachita. Mwanayo amaona machimowo koma sawachita.+