2 Mbiri 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake. Yeremiya 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Pita ukauze Zedekiya mfumu ya Yuda,+ kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ine ndikupereka mzinda uwu m’manja mwa mfumu ya Babulo+ ndipo idzautentha.+
17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake.
2 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Pita ukauze Zedekiya mfumu ya Yuda,+ kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ine ndikupereka mzinda uwu m’manja mwa mfumu ya Babulo+ ndipo idzautentha.+