Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Nthawi yonseyi Elisa anali kuona zimene zinali kuchitikazo, ndipo anali kufuula kuti: “Bambo anga, bambo anga!+ Galeta lankhondo la Isiraeli ndi okwera mahatchi ake!”+ Zitatero, Elisa sanamuonenso Eliya. Kenako Elisa anagwira zovala zake n’kuzing’amba pakati.+

  • 2 Mafumu 6:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mfumu ya Isiraeli itangoona anthuwo, inafunsa Elisa kuti: “Kodi ndiwaphe?+ Ndiwaphe kodi bambo?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena