2 Mafumu 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano atumiki ake anamutsatira ndipo anamufunsa kuti: “Bambo wanga,+ kodi mneneriyo akanakuuzani kuti muchite chinthu chachikulu, simukanachita? Nanga bwanji poti wangokuuzani kuti, ‘Kasambeni ndi kuyeretsedwa’?” Machitidwe 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Sitefano anati: “Amuna inu, abale anga ndi abambo anga, mvetserani! Mulungu waulemerero+ anaonekera kwa kholo lathu Abulahamu pamene anali ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harana.+ 1 Akorinto 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti ngakhale mutakhala ndi aphunzitsi+ 10,000 mwa Khristu, ndithudi mulibe abambo ambiri,+ pakuti mwa Khristu Yesu ndakhala bambo anu kudzera mwa uthenga wabwino.+
13 Tsopano atumiki ake anamutsatira ndipo anamufunsa kuti: “Bambo wanga,+ kodi mneneriyo akanakuuzani kuti muchite chinthu chachikulu, simukanachita? Nanga bwanji poti wangokuuzani kuti, ‘Kasambeni ndi kuyeretsedwa’?”
2 Sitefano anati: “Amuna inu, abale anga ndi abambo anga, mvetserani! Mulungu waulemerero+ anaonekera kwa kholo lathu Abulahamu pamene anali ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harana.+
15 Pakuti ngakhale mutakhala ndi aphunzitsi+ 10,000 mwa Khristu, ndithudi mulibe abambo ambiri,+ pakuti mwa Khristu Yesu ndakhala bambo anu kudzera mwa uthenga wabwino.+