2 Mbiri 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Panali anthu ambiri ochokera ku Efuraimu,+ ku Manase,+ ku Isakara ndi ku Zebuloni+ amene sanadziyeretse+ ndipo anadya pasikayo mosatsatira zimene zinalembedwa.+ Koma Hezekiya anawapempherera+ kuti: “Yehova wabwino+ asakwiyire 2 Mbiri 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 aliyense amene wakonza mtima wake+ kuti afunefune Mulungu woona Yehova, Mulungu wa makolo ake, ngakhale kuti sanadziyeretse mogwirizana ndi zinthu zopatulika.”+
18 Panali anthu ambiri ochokera ku Efuraimu,+ ku Manase,+ ku Isakara ndi ku Zebuloni+ amene sanadziyeretse+ ndipo anadya pasikayo mosatsatira zimene zinalembedwa.+ Koma Hezekiya anawapempherera+ kuti: “Yehova wabwino+ asakwiyire
19 aliyense amene wakonza mtima wake+ kuti afunefune Mulungu woona Yehova, Mulungu wa makolo ake, ngakhale kuti sanadziyeretse mogwirizana ndi zinthu zopatulika.”+