1 Mafumu 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi mbuye wanga simunamve zimene ndinachita pamene Yezebeli anapha aneneri a Yehova? Ndinabisa aneneri 100 a Yehova m’phanga.+ Ndinawagawa m’magulu awiri a aneneri 50 gulu lililonse, ndipo ndinali kuwapatsa mkate ndi madzi.+ 1 Mafumu 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno mupeze anthu awiri+ opanda pake+ adzakhale patsogolo pake ndi kupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja ndi kum’ponya miyala kuti afe.”+
13 Kodi mbuye wanga simunamve zimene ndinachita pamene Yezebeli anapha aneneri a Yehova? Ndinabisa aneneri 100 a Yehova m’phanga.+ Ndinawagawa m’magulu awiri a aneneri 50 gulu lililonse, ndipo ndinali kuwapatsa mkate ndi madzi.+
10 Ndiyeno mupeze anthu awiri+ opanda pake+ adzakhale patsogolo pake ndi kupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja ndi kum’ponya miyala kuti afe.”+