2 Mafumu 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Ataliya,+ mayi wa Ahaziya+ ataona kuti mwana wake wafa, anapha ana onse achifumu.+ 2 Mafumu 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anapitiriza kubisidwa m’nyumba ya Yehova zaka 6, pamene Ataliya anali kulamulira dzikolo.+