2 Mbiri 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anapitiriza kubisidwa m’nyumba ya Mulungu woona zaka 6,+ pamene Ataliya+ anali mfumukazi ya dzikolo.+ Salimo 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu oipa akuyendayenda ponseponse,Chifukwa ana a anthu amayamikira zoipa.+ Yesaya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Amene amagawira anthu anga ntchito, akuwagwiritsa ntchito mwankhanza, ndipo akazi ndi amene akuwalamulira.+ Inu anthu anga, amene akukutsogolerani akukusocheretsani,+ ndipo asokoneza njira yanu.+ Malaki 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Panopa anthu odzikuza tikuwatcha odala.+ Komanso anthu ochita zoipa zinthu zikuwayendera bwino.+ Iwo ayesa Mulungu koma sakulandira chilango.’”+ 1 Timoteyo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sindikuvomereza kuti mkazi aziphunzitsa+ kapena kukhala ndi ulamuliro pa mwamuna,+ koma azikhala chete.
12 Anapitiriza kubisidwa m’nyumba ya Mulungu woona zaka 6,+ pamene Ataliya+ anali mfumukazi ya dzikolo.+
12 Amene amagawira anthu anga ntchito, akuwagwiritsa ntchito mwankhanza, ndipo akazi ndi amene akuwalamulira.+ Inu anthu anga, amene akukutsogolerani akukusocheretsani,+ ndipo asokoneza njira yanu.+
15 Panopa anthu odzikuza tikuwatcha odala.+ Komanso anthu ochita zoipa zinthu zikuwayendera bwino.+ Iwo ayesa Mulungu koma sakulandira chilango.’”+
12 Sindikuvomereza kuti mkazi aziphunzitsa+ kapena kukhala ndi ulamuliro pa mwamuna,+ koma azikhala chete.