Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 5:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Aneneri akulosera monama,+ ndipo ansembe akupondereza anthu ndi mphamvu zawo.+ Anthu anga nawonso akukonda zimenezi.+ Ndipo kodi anthu inu mudzachita chiyani pamapeto pake?”+

  • Habakuku 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Choncho lamulo latha mphamvu ndipo anthu sakuchitanso chilungamo.+ Chilungamo chapotozedwa chifukwa anthu oipa akupondereza anthu olungama.+

  • Mateyu 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Alekeni amenewo. Iwo ndi atsogoleri akhungu. Chotero ngati munthu wakhungu akutsogolera wakhungu mnzake, onse awiri adzagwera m’dzenje.”+

  • Mateyu 23:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Tsoka kwa inu alembi ndi Afarisi, onyenga inu!+ Chifukwa mumatha mitunda kuti mukatembenuze munthu mmodzi, koma akatembenuka mumam’sandutsa woyenera kuponyedwa m’Gehena* kuposa inuyo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena