2 Mafumu 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Ataliya,+ mayi wa Ahaziya+ ataona kuti mwana wake wafa, anapha ana onse achifumu.+ Nahumu 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Taona! Anthu ako ali ngati akazi.+ Zipata za dziko lako zidzatsegulidwa kuti adani ako alowemo. Moto udzanyeketsa mipiringidzo ya mzinda wako.+ 1 Timoteyo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sindikuvomereza kuti mkazi aziphunzitsa+ kapena kukhala ndi ulamuliro pa mwamuna,+ koma azikhala chete.
13 “Taona! Anthu ako ali ngati akazi.+ Zipata za dziko lako zidzatsegulidwa kuti adani ako alowemo. Moto udzanyeketsa mipiringidzo ya mzinda wako.+
12 Sindikuvomereza kuti mkazi aziphunzitsa+ kapena kukhala ndi ulamuliro pa mwamuna,+ koma azikhala chete.