Yesaya 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’tsiku limenelo, Aiguputo adzakhala ngati akazi. Iwo adzanjenjemera+ ndi kuchita mantha, chifukwa Yehova wa makamu adzawatambasulira dzanja lake.+ Yeremiya 51:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Amuna amphamvu a ku Babulo asiya kumenya nkhondo. Iwo angokhala m’malo otetezeka. Mphamvu zawo zatha.+ Akhala ngati akazi.+ Nyumba za m’Babulo zatenthedwa. Mipiringidzo yake yathyoledwa.+
16 M’tsiku limenelo, Aiguputo adzakhala ngati akazi. Iwo adzanjenjemera+ ndi kuchita mantha, chifukwa Yehova wa makamu adzawatambasulira dzanja lake.+
30 “Amuna amphamvu a ku Babulo asiya kumenya nkhondo. Iwo angokhala m’malo otetezeka. Mphamvu zawo zatha.+ Akhala ngati akazi.+ Nyumba za m’Babulo zatenthedwa. Mipiringidzo yake yathyoledwa.+