Yoswa 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zimene zichitike n’zakuti, mapazi a ansembe onyamula likasa la Yehova, Ambuye wa dziko lonse lapansi, akangoponda m’madzi, madzi a mtsinje wa Yorodanowo aduka. Madzi otsika kuchokera kumtunda aima n’kukhala damu limodzi.”+ 2 Mafumu 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Eliya anatenga chovala chake chauneneri+ n’kuchipinda. Atatero anamenya nacho madzi a mtsinjewo, ndipo pang’onopang’ono madzi onsewo anagawanika uku ndi uku, chotero iwo anawoloka pouma.+
13 Zimene zichitike n’zakuti, mapazi a ansembe onyamula likasa la Yehova, Ambuye wa dziko lonse lapansi, akangoponda m’madzi, madzi a mtsinje wa Yorodanowo aduka. Madzi otsika kuchokera kumtunda aima n’kukhala damu limodzi.”+
8 Kenako Eliya anatenga chovala chake chauneneri+ n’kuchipinda. Atatero anamenya nacho madzi a mtsinjewo, ndipo pang’onopang’ono madzi onsewo anagawanika uku ndi uku, chotero iwo anawoloka pouma.+