1 Mafumu 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Yehova anamuuza kuti: “Nyamuka, bwerera udzere kuchipululu cha Damasiko.+ Pita ukadzoze+ Hazaeli+ kuti akhale mfumu ya Siriya. 2 Mafumu 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 M’masiku amenewo, Yehova anayamba kulanda dziko la Isiraeli pang’ono ndi pang’ono, ndipo Hazaeli+ anapitiriza kupha anthu m’madera onse a dziko la Isiraeli.
15 Kenako Yehova anamuuza kuti: “Nyamuka, bwerera udzere kuchipululu cha Damasiko.+ Pita ukadzoze+ Hazaeli+ kuti akhale mfumu ya Siriya.
32 M’masiku amenewo, Yehova anayamba kulanda dziko la Isiraeli pang’ono ndi pang’ono, ndipo Hazaeli+ anapitiriza kupha anthu m’madera onse a dziko la Isiraeli.