Salimo 96:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mtunda ukondwere ndi zonse zimene zili kumeneko.+Pa nthawi imodzimodziyo, mitengo ya m’nkhalango ifuule mokondwera pamaso pa Yehova.+ Yesaya 55:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Pakuti anthu inu mudzachoka ndi chisangalalo+ ndipo mudzafika ndi mtendere.+ Mapiri ndi zitunda zidzakusangalalirani ndi mfuu yachisangalalo,+ ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba m’manja.+
12 Mtunda ukondwere ndi zonse zimene zili kumeneko.+Pa nthawi imodzimodziyo, mitengo ya m’nkhalango ifuule mokondwera pamaso pa Yehova.+ Yesaya 55:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Pakuti anthu inu mudzachoka ndi chisangalalo+ ndipo mudzafika ndi mtendere.+ Mapiri ndi zitunda zidzakusangalalirani ndi mfuu yachisangalalo,+ ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba m’manja.+
12 “Pakuti anthu inu mudzachoka ndi chisangalalo+ ndipo mudzafika ndi mtendere.+ Mapiri ndi zitunda zidzakusangalalirani ndi mfuu yachisangalalo,+ ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba m’manja.+