Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 16:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Pa nthawi imodzimodziyo, mitengo ya m’nkhalango ifuule mokondwera chifukwa cha Yehova,+

      Pakuti iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+

  • Salimo 148:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Mutamandeni inu mapiri ndi inu nonse zitunda,+

      Inu mitengo ya zipatso ndi inu nonse mitengo ya mkungudza.+

  • Yesaya 55:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Pakuti anthu inu mudzachoka ndi chisangalalo+ ndipo mudzafika ndi mtendere.+ Mapiri ndi zitunda zidzakusangalalirani ndi mfuu yachisangalalo,+ ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba m’manja.+

  • Ezekieli 34:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mtengo wam’munda udzabereka zipatso.+ Nthaka idzatulutsa zokolola zake.+ Iwo adzakhala m’dziko lawo mwabata.+ Ndikadzathyola goli lawo+ ndi kuwapulumutsa m’dzanja la amene anali kuwagwiritsa ntchito monga akapolo,+ adzadziwa kuti ine ndine Yehova.

  • Ezekieli 36:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndidzachulukitsa zipatso za mtengo ndi zokolola zakumunda kuti musadzanyozekenso chifukwa cha njala pakati pa mitundu ina ya anthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena