2 Samueli 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ku chiyambi kwa chaka,+ pa nthawi imene mafumu anali kupita kukamenya nkhondo,+ Davide anatumiza Yowabu, atumiki ake ndi Isiraeli yense kuti akawononge ana a Amoni+ ndi kuzungulira mzinda wa Raba.+ Koma Davide anatsalira ku Yerusalemu. Mlaliki 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nthawi ya chikondi ndi nthawi ya chidani ndi munthu.+ Nthawi yankhondo+ ndi nthawi yamtendere.+
11 Ndiyeno ku chiyambi kwa chaka,+ pa nthawi imene mafumu anali kupita kukamenya nkhondo,+ Davide anatumiza Yowabu, atumiki ake ndi Isiraeli yense kuti akawononge ana a Amoni+ ndi kuzungulira mzinda wa Raba.+ Koma Davide anatsalira ku Yerusalemu.