1 Samueli 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngoloyo inafika m’munda wa Yoswa, amene kwawo kunali ku Beti-semesi, ndi kuima pamalo pamene panali mwala waukulu. Ndiyeno anthuwo anawaza matabwa a ngoloyo ndipo ng’ombezo+ anazipereka nsembe yopsereza kwa Yehova.+ 1 Mafumu 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho anabwerera n’kutenga ng’ombe zamphongo ziwiri n’kuzipha.*+ Anatenga mitengo ya pulawo+ ya ng’ombezo n’kuphikira nyama yake. Kenako anaipereka kwa anthu kuti adye. Atatero, iye ananyamuka n’kutsatira Eliya ndipo anayamba kum’tumikira.+
14 Ngoloyo inafika m’munda wa Yoswa, amene kwawo kunali ku Beti-semesi, ndi kuima pamalo pamene panali mwala waukulu. Ndiyeno anthuwo anawaza matabwa a ngoloyo ndipo ng’ombezo+ anazipereka nsembe yopsereza kwa Yehova.+
21 Choncho anabwerera n’kutenga ng’ombe zamphongo ziwiri n’kuzipha.*+ Anatenga mitengo ya pulawo+ ya ng’ombezo n’kuphikira nyama yake. Kenako anaipereka kwa anthu kuti adye. Atatero, iye ananyamuka n’kutsatira Eliya ndipo anayamba kum’tumikira.+