Ekisodo 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mundipangire guwa lansembe ladothi,+ ndipo muziperekapo nsembe zanu zopsereza ndi nsembe zachiyanjano,* nkhosa zanu ndi ng’ombe zanu.+ M’malo onse amene ndidzachititsa dzina langa kukumbukika ndidzabwera kwa inu ndipo ndidzakudalitsani ndithu.+ Oweruza 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka m’mawa kwambiri ndi kumanga guwa lansembe pamenepo, ndipo anapereka nsembe zopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano.+
24 Mundipangire guwa lansembe ladothi,+ ndipo muziperekapo nsembe zanu zopsereza ndi nsembe zachiyanjano,* nkhosa zanu ndi ng’ombe zanu.+ M’malo onse amene ndidzachititsa dzina langa kukumbukika ndidzabwera kwa inu ndipo ndidzakudalitsani ndithu.+
4 Ndiyeno tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka m’mawa kwambiri ndi kumanga guwa lansembe pamenepo, ndipo anapereka nsembe zopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano.+