2 Mbiri 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehoasi anatenga golide ndi siliva yense, ndi ziwiya zonse zimene anazipeza m’nyumba ya Mulungu woona, ndipo anatenganso Obedi-edomu+ ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Anagwiranso anthu ena n’kubwerera ku Samariya.+
24 Yehoasi anatenga golide ndi siliva yense, ndi ziwiya zonse zimene anazipeza m’nyumba ya Mulungu woona, ndipo anatenganso Obedi-edomu+ ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Anagwiranso anthu ena n’kubwerera ku Samariya.+