1 Mbiri 2:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Awa ndiwo anali ana a Kalebe. Tsopano awa ndiwo ana a Hura+ mwana woyamba wa Efurata:+ Sobala+ bambo wa Kiriyati-yearimu,+ 1 Mbiri 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Penueli bambo wa Gedori,+ ndi Ezeri bambo wa Husa. Amenewa ndiwo anali ana a Hura+ mwana woyamba wa Efurata, ndipo Hura anali bambo wa Betelehemu.+
50 Awa ndiwo anali ana a Kalebe. Tsopano awa ndiwo ana a Hura+ mwana woyamba wa Efurata:+ Sobala+ bambo wa Kiriyati-yearimu,+
4 Penueli bambo wa Gedori,+ ndi Ezeri bambo wa Husa. Amenewa ndiwo anali ana a Hura+ mwana woyamba wa Efurata, ndipo Hura anali bambo wa Betelehemu.+