-
1 Mbiri 22:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Zitatha izi, Davide analamula akalonga onse a Isiraeli kuti athandize mwana wake Solomo. Iye anati:
-
-
1 Mbiri 28:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Davide anasonkhanitsa akalonga onse+ a Isiraeli ku Yerusalemu. Akalongawo+ anali a mafuko ndi a magulu otumikira mfumu, atsogoleri a magulu a anthu 1,000,+ atsogoleri a magulu a anthu 100,+ ndiponso atsogoleri oyang’anira katundu yense+ ndi ziweto+ za mfumu ndi za ana ake.+ Panalinso nduna za panyumba ya mfumu+ ndi amuna amphamvu,+ ngakhale mwamuna aliyense wamphamvu ndi wolimba mtima.
-