Deuteronomo 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muzikumbukira Yehova Mulungu wanu, chifukwa ndiye amakupatsani mphamvu kuti mupeze chuma,+ pofuna kusunga pangano lake limene analumbirira makolo anu, monga mmene wachitira lero.+ Miyambo 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Madalitso a Yehova ndi amene amalemeretsa,+ ndipo sawonjezerapo ululu.+ Afilipi 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nayenso Mulungu wanga+ adzakupatsani zosowa zanu zonse+ mogwirizana ndi kuchuluka kwa chuma chake+ chaulemerero, kudzera mwa Khristu Yesu.
18 Muzikumbukira Yehova Mulungu wanu, chifukwa ndiye amakupatsani mphamvu kuti mupeze chuma,+ pofuna kusunga pangano lake limene analumbirira makolo anu, monga mmene wachitira lero.+
19 Nayenso Mulungu wanga+ adzakupatsani zosowa zanu zonse+ mogwirizana ndi kuchuluka kwa chuma chake+ chaulemerero, kudzera mwa Khristu Yesu.