Ekisodo 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo ana aamuna a Uziyeli anali Misayeli, Elizafana ndi Sitiri.+ Levitiko 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zitatero, Mose anaitana Misayeli ndi Elizafana, ana a Uziyeli,+ bambo aang’ono a Aroni, n’kuwauza kuti: “Bwerani muchotse abale anu patsogolo pa malo oyera, mupite nawo kunja kwa msasa.”+ 1 Mbiri 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa ana a Uziyeli+ panali Aminadabu mtsogoleri wawo ndi abale ake okwanira 112.
4 Zitatero, Mose anaitana Misayeli ndi Elizafana, ana a Uziyeli,+ bambo aang’ono a Aroni, n’kuwauza kuti: “Bwerani muchotse abale anu patsogolo pa malo oyera, mupite nawo kunja kwa msasa.”+