Yoswa 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mizinda yotsatirayi ya m’gawo la Isakara ndi Aseri, pamodzi ndi anthu ake ndi midzi yake yozungulira, inali ya Manase:+ Beti-seani,+ Ibuleamu,+ Dori,+ Eni-dori,+ Taanaki,+ ndi Megido.+ Madera atatu amapiri analinso ake. 1 Samueli 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamapeto pake, anakaika zida zakezo+ m’nyumba ya zifaniziro za Asitoreti,+ ndipo anapachika mtembo wake pakhoma mumzinda wa Beti-sani.+
11 Mizinda yotsatirayi ya m’gawo la Isakara ndi Aseri, pamodzi ndi anthu ake ndi midzi yake yozungulira, inali ya Manase:+ Beti-seani,+ Ibuleamu,+ Dori,+ Eni-dori,+ Taanaki,+ ndi Megido.+ Madera atatu amapiri analinso ake.
10 Pamapeto pake, anakaika zida zakezo+ m’nyumba ya zifaniziro za Asitoreti,+ ndipo anapachika mtembo wake pakhoma mumzinda wa Beti-sani.+