Oweruza 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mafumu anabwera ndi kumenya nkhondo.Pamenepo mafumu a Kanani anamenya nkhondo,+Anamenya nkhondo ku Taanaki,+ pafupi ndi madzi a ku Megido.+Iwo sanapezepo phindu la siliva.+ 1 Mafumu 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Baana mwana wa Ahiludi, ku Taanaki+ ndi ku Megido+ ndi ku Beti-seani+ konse, pafupi ndi Zeretani+ kumunsi kwa Yezereeli,+ kuchokera ku Beti-seani kukafika ku Abele-mehola+ mpaka kuchigawo cha Yokimeamu,+
19 Mafumu anabwera ndi kumenya nkhondo.Pamenepo mafumu a Kanani anamenya nkhondo,+Anamenya nkhondo ku Taanaki,+ pafupi ndi madzi a ku Megido.+Iwo sanapezepo phindu la siliva.+
12 Baana mwana wa Ahiludi, ku Taanaki+ ndi ku Megido+ ndi ku Beti-seani+ konse, pafupi ndi Zeretani+ kumunsi kwa Yezereeli,+ kuchokera ku Beti-seani kukafika ku Abele-mehola+ mpaka kuchigawo cha Yokimeamu,+