1 Mbiri 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kumbali ya Alevi, Ahiya anali kuyang’anira chuma+ cha m’nyumba ya Mulungu woona, ndi chuma cha zinthu zimene anaziyeretsa kukhala zopatulika.+ 2 Mbiri 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthuwo anapitiriza kubweretsa zopereka,+ chakhumi,+ ndi zinthu zopatulika. Iwo ankabweretsa zimenezi mokhulupirika.+ Konaniya Mlevi ndiye anali kuyang’anira monga mtsogoleri, ndipo Simeyi m’bale wake anali wachiwiri wake.
20 Kumbali ya Alevi, Ahiya anali kuyang’anira chuma+ cha m’nyumba ya Mulungu woona, ndi chuma cha zinthu zimene anaziyeretsa kukhala zopatulika.+
12 Anthuwo anapitiriza kubweretsa zopereka,+ chakhumi,+ ndi zinthu zopatulika. Iwo ankabweretsa zimenezi mokhulupirika.+ Konaniya Mlevi ndiye anali kuyang’anira monga mtsogoleri, ndipo Simeyi m’bale wake anali wachiwiri wake.