1 Mafumu 7:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pa mapeto pake, Mfumu Solomo inamaliza+ ntchito yonse yokhudza nyumba ya Yehova imene inayenera kugwira. Kenako Solomo anayamba kubweretsa zinthu zonse zimene Davide bambo ake+ anaziyeretsa. Anatenga siliva, golide, ndi ziwiya zina n’kukaziika mosungira chuma cha panyumba ya Yehova.+ 1 Mbiri 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zinthu zimenezi Mfumu Davide inazipatulira+ Yehova pamodzi ndi siliva ndi golide amene inalanda ku mitundu yonse,+ kuchokera ku Edomu, ku Mowabu,+ kwa ana a Amoni,+ Afilisiti,+ ndi Aamaleki.+
51 Pa mapeto pake, Mfumu Solomo inamaliza+ ntchito yonse yokhudza nyumba ya Yehova imene inayenera kugwira. Kenako Solomo anayamba kubweretsa zinthu zonse zimene Davide bambo ake+ anaziyeretsa. Anatenga siliva, golide, ndi ziwiya zina n’kukaziika mosungira chuma cha panyumba ya Yehova.+
11 Zinthu zimenezi Mfumu Davide inazipatulira+ Yehova pamodzi ndi siliva ndi golide amene inalanda ku mitundu yonse,+ kuchokera ku Edomu, ku Mowabu,+ kwa ana a Amoni,+ Afilisiti,+ ndi Aamaleki.+