2 Samueli 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nkhondo ya pakati pa nyumba ya Sauli ndi nyumba ya Davide inatenga nthawi yaitali.+ Davide anapitirizabe kukhala wamphamvu+ koma nyumba ya Sauli inali kufookerafookera.+ 2 Samueli 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero ulamuliro wa Davide unakulirakulira,+ ndipo Yehova Mulungu wa makamu+ anali naye.+
3 Nkhondo ya pakati pa nyumba ya Sauli ndi nyumba ya Davide inatenga nthawi yaitali.+ Davide anapitirizabe kukhala wamphamvu+ koma nyumba ya Sauli inali kufookerafookera.+