2 Samueli 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho ngakhale mwamuna wolimba mtima amene ali ndi mtima ngati wa mkango+ adzafooka+ ndithu. Izi zili choncho chifukwa Isiraeli yense akudziwa kuti bambo wako ndi mwamuna wamphamvu,+ ngatinso mmene alili amuna olimba mtima amene ali naye.+
10 Choncho ngakhale mwamuna wolimba mtima amene ali ndi mtima ngati wa mkango+ adzafooka+ ndithu. Izi zili choncho chifukwa Isiraeli yense akudziwa kuti bambo wako ndi mwamuna wamphamvu,+ ngatinso mmene alili amuna olimba mtima amene ali naye.+