2 Samueli 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo Davide anafunsira+ kwa Yehova ndipo anamuyankha kuti: “Ayi usapite. Koma uwazembere kumbuyo kwawo ndi kuwaukira kutsogolo kwa zitsamba za baka.*+ Miyambo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Uzim’kumbukira m’njira zako zonse,+ ndipo iye adzawongola njira zako.+
23 Pamenepo Davide anafunsira+ kwa Yehova ndipo anamuyankha kuti: “Ayi usapite. Koma uwazembere kumbuyo kwawo ndi kuwaukira kutsogolo kwa zitsamba za baka.*+