1 Mbiri 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo Davide anafunsiranso+ kwa Mulungu ndipo Mulungu woonayo anamuyankha kuti: “Ayi usapite kukakumana nawo. Koma uwazembere ndipo ukawaukire kutsogolo kwa zitsamba za baka.*+ Salimo 84:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Poyenda m’chigwa chouma mmene muli zitsamba za baka,*+Amasandutsa chigwacho kukhala choyenda madzi ochokera pakasupe,Mlangizi wafunda mawu otamanda.+
14 Pamenepo Davide anafunsiranso+ kwa Mulungu ndipo Mulungu woonayo anamuyankha kuti: “Ayi usapite kukakumana nawo. Koma uwazembere ndipo ukawaukire kutsogolo kwa zitsamba za baka.*+
6 Poyenda m’chigwa chouma mmene muli zitsamba za baka,*+Amasandutsa chigwacho kukhala choyenda madzi ochokera pakasupe,Mlangizi wafunda mawu otamanda.+