1 Samueli 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndithamangitse gulu la achifwambali? Kodi ndiwapeza?” Pamenepo anamuyankha+ kuti: “Inde athamangitse chifukwa uwapezadi ndi kulanditsa zinthu zimene afunkha.”+ 2 Samueli 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Davide anafunsira+ kwa Yehova kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi muwapereka m’manja mwanga?” Pamenepo Yehova anauza Davide kuti: “Pita, ndipereka ndithu Afilisitiwa m’manja mwako.”+ Miyambo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khulupirira Yehova ndi mtima wako wonse,+ ndipo usadalire luso lako lomvetsa zinthu.+
8 Ndiyeno Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndithamangitse gulu la achifwambali? Kodi ndiwapeza?” Pamenepo anamuyankha+ kuti: “Inde athamangitse chifukwa uwapezadi ndi kulanditsa zinthu zimene afunkha.”+
19 Ndiyeno Davide anafunsira+ kwa Yehova kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi muwapereka m’manja mwanga?” Pamenepo Yehova anauza Davide kuti: “Pita, ndipereka ndithu Afilisitiwa m’manja mwako.”+