Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 27:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Yoswayo aziimirira pamaso pa wansembe Eleazara, ndipo Eleazara azifunsira+ chigamulo cha Yehova m’malo mwa Yoswayo pogwiritsa ntchito maere a Urimu.+ Yoswa akalamula, ana onse a Isiraeli ndi khamu lonse azituluka naye, ndipo akalamulanso, onsewo azibwerako limodzi naye.”

  • Oweruza 18:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno iwo anamuuza kuti: “Tifunsire+ kwa Mulungu+ kuti tidziwe ngati kumene tikupita tidzayendako bwino.”

  • Oweruza 20:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Masiku amenewo Pinihasi,+ mwana wa Eleazara, mwana wa Aroni, ndiye anali kuimirira pafupi ndi likasalo.+ Chotero iye anafunsa kuti: “Kodi ndipitenso kukamenyana ndi ana a m’bale wanga Benjamini kapena ndisapite?”+ Poyankha, Yehova anati: “Pita, chifukwa mawa ndim’pereka m’dzanja lako.”+

  • 1 Samueli 23:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Davide anayamba kufunsira+ kwa Yehova, kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa?” Yehova anayankha Davide kuti: “Pita, ukamenyane ndi Afilisitiwo ndipo ukapulumutse Keila.”

  • 1 Samueli 23:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kodi anthu a mumzinda wa Keila adzandipereka m’manja mwake? Kodi Sauli abweradi kuno monga mmene ine mtumiki wanu ndamvera? Yehova Mulungu wa Isiraeli, ndiuzeni ine mtumiki wanu, chonde.” Pamenepo Yehova anamuyankha kuti: “Abweradi kuno.”+

  • 1 Samueli 28:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ngakhale kuti anali kufunsira kwa Yehova,+ Yehova sanamuyankhe+ kaya kudzera m’maloto,+ Urimu+ kapena kudzera mwa aneneri.+

  • Miyambo 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Khulupirira Yehova ndi mtima wako wonse,+ ndipo usadalire luso lako lomvetsa zinthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena