1 Mafumu 22:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Nkhondoyo inafika poopsa tsiku limenelo, ndipo mfumuyo anaiimiritsa m’galeta moyang’anizana ndi Asiriya. Potsirizira pake inafa+ madzulo, ndipo magazi ochokera pachilonda chake anali kuyenderera mkati mwa galeta lankhondolo.+ 2 Mbiri 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho Yehova waika mzimu wabodza m’kamwa mwa aneneri anuwa,+ koma Yehovayo wanena kuti inuyo muona tsoka.”+
35 Nkhondoyo inafika poopsa tsiku limenelo, ndipo mfumuyo anaiimiritsa m’galeta moyang’anizana ndi Asiriya. Potsirizira pake inafa+ madzulo, ndipo magazi ochokera pachilonda chake anali kuyenderera mkati mwa galeta lankhondolo.+
22 Choncho Yehova waika mzimu wabodza m’kamwa mwa aneneri anuwa,+ koma Yehovayo wanena kuti inuyo muona tsoka.”+