1 Mafumu 20:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Tsopano mneneriyo anauza mfumuyo kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Popeza wamasula munthu woyenera kuwonongedwa ndi ine,+ moyo wako ulowa m’malo mwake+ ndipo anthu ako alowa m’malo mwa anthu ake.’”+ 2 Mbiri 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nkhondoyo inafika poopsa tsiku limenelo, ndipo mfumu ya Isiraeliyo anaiimiritsa m’galeta moyang’anizana ndi Asiriya mpaka madzulo. Potsirizira pake mfumuyo inafa pamene dzuwa linali kulowa.+
42 Tsopano mneneriyo anauza mfumuyo kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Popeza wamasula munthu woyenera kuwonongedwa ndi ine,+ moyo wako ulowa m’malo mwake+ ndipo anthu ako alowa m’malo mwa anthu ake.’”+
34 Nkhondoyo inafika poopsa tsiku limenelo, ndipo mfumu ya Isiraeliyo anaiimiritsa m’galeta moyang’anizana ndi Asiriya mpaka madzulo. Potsirizira pake mfumuyo inafa pamene dzuwa linali kulowa.+