Yoswa 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.” Oweruza 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano masiku amenewo, mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Ndiyeno Mlevi wina anakhala kwa kanthawi m’dera lamapiri lakutali kwambiri la Efuraimu.+ Patapita nthawi, anatenga mkazi wa ku Betelehemu,+ ku Yuda, kukhala mdzakazi wake.+
15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.”
19 Tsopano masiku amenewo, mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Ndiyeno Mlevi wina anakhala kwa kanthawi m’dera lamapiri lakutali kwambiri la Efuraimu.+ Patapita nthawi, anatenga mkazi wa ku Betelehemu,+ ku Yuda, kukhala mdzakazi wake.+