Yoswa 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.” Yoswa 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako ana a Yosefe anati: “Dera lamapiri silitikwanira, ndiponso Akanani a kuchigwa, a ku Beti-seani+ ndi midzi yake yozungulira, ndiponso a kuchigwa cha Yezereeli,+ ali ndi magaleta ankhondo+ okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa za m’mawilo.”
15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.”
16 Kenako ana a Yosefe anati: “Dera lamapiri silitikwanira, ndiponso Akanani a kuchigwa, a ku Beti-seani+ ndi midzi yake yozungulira, ndiponso a kuchigwa cha Yezereeli,+ ali ndi magaleta ankhondo+ okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa za m’mawilo.”