Yoswa 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Malire a gawo lawo anakafika ku Yezereeli,+ Kesulotu, Sunemu,+ Oweruza 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno Amidiyani+ ndi Aamaleki onse,+ pamodzi ndi anthu onse a Kum’mawa+ anasonkhana pamodzi+ ndi kuwoloka mtsinje, ndipo anamanga msasa wawo m’chigwa cha Yezereeli.+
33 Ndiyeno Amidiyani+ ndi Aamaleki onse,+ pamodzi ndi anthu onse a Kum’mawa+ anasonkhana pamodzi+ ndi kuwoloka mtsinje, ndipo anamanga msasa wawo m’chigwa cha Yezereeli.+