5 Kuwonjezera pamenepo, ndidzafunsa za magazi anu. Ngati magazi anu akhetsedwa ndi chamoyo chilichonse, chamoyocho chiyenera kuphedwa, ndipo ngati moyo wa munthu wachotsedwa ndi munthu mnzake ndidzaufuna kuchokera kwa iye.+
51 Kuyambira magazi a Abele+ mpaka magazi a Zekariya,+ amene anaphedwa pakati pa guwa lansembe ndi nyumba yopatulika.’+ Inde, ndikukuuzani, m’badwo uwu udzafunsidwa za magazi amenewo.