Ekisodo 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Asakhale m’dziko lako, kuti asakuchimwitse pamaso panga. Ukatumikira milungu yawo, umenewo udzakhala msampha kwa iwe.”+ Deuteronomo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muwononge anthu a mitundu yonse amene Yehova Mulungu wanu akuwapereka kwa inu.+ Musawamvere chisoni+ ndipo musatumikire milungu yawo+ chifukwa kuchita zimenezo kudzakutcherani msampha.+ Yesaya 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kuwonongeka kwa opanduka ndi kwa ochimwa kudzachitikira limodzi,+ ndipo anthu omusiya Yehova adzatha.+
33 Asakhale m’dziko lako, kuti asakuchimwitse pamaso panga. Ukatumikira milungu yawo, umenewo udzakhala msampha kwa iwe.”+
16 Muwononge anthu a mitundu yonse amene Yehova Mulungu wanu akuwapereka kwa inu.+ Musawamvere chisoni+ ndipo musatumikire milungu yawo+ chifukwa kuchita zimenezo kudzakutcherani msampha.+
28 Kuwonongeka kwa opanduka ndi kwa ochimwa kudzachitikira limodzi,+ ndipo anthu omusiya Yehova adzatha.+