Salimo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amadziwa njira za olungama,+Koma oipa adzatheratu pamodzi ndi njira zawo.+ Salimo 37:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma anthu onse ochimwa adzafafanizidwa.+M’tsogolo, anthu oipa adzaphedwa.+ Salimo 104:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ochimwa adzafafanizidwa padziko lapansi.+Ndipo anthu oipa sadzakhalaponso.+Tamanda Yehova, iwe moyo wanga. Tamandani Ya, anthu inu!*+ Miyambo 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu wodzudzulidwa kawirikawiri+ koma amene amaumitsa khosi lake,+ adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo akadzatero sadzachira.+ Ezekieli 20:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndidzachotsa pakati panu anthu ondipandukira ndi ondichimwira.+ Pakuti ndidzawatulutsa m’dziko limene akukhalamo monga alendo, koma sadzalowa m’dziko la Isiraeli,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+ 2 Petulo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo mwa mawu amodzimodziwo, kumwamba+ kumene kulipo panopa limodzi ndi dziko lapansi,+ azisungira moto+ m’tsiku lachiweruzo+ ndi chiwonongeko cha anthu osaopa Mulungu.+
35 Ochimwa adzafafanizidwa padziko lapansi.+Ndipo anthu oipa sadzakhalaponso.+Tamanda Yehova, iwe moyo wanga. Tamandani Ya, anthu inu!*+
29 Munthu wodzudzulidwa kawirikawiri+ koma amene amaumitsa khosi lake,+ adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo akadzatero sadzachira.+
38 Ndidzachotsa pakati panu anthu ondipandukira ndi ondichimwira.+ Pakuti ndidzawatulutsa m’dziko limene akukhalamo monga alendo, koma sadzalowa m’dziko la Isiraeli,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+
7 Ndipo mwa mawu amodzimodziwo, kumwamba+ kumene kulipo panopa limodzi ndi dziko lapansi,+ azisungira moto+ m’tsiku lachiweruzo+ ndi chiwonongeko cha anthu osaopa Mulungu.+