Ekisodo 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zitatero Mose anati: “Dzilimbitseni* lero kuti muchite utumiki kwa Yehova,+ chifukwa aliyense wa inu waukira mwana wake ndi m’bale wake,+ kuti Mulungu akupatseni dalitso lero.”+ Levitiko 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kwa masiku 7,+ kufikira tsiku lomaliza la kulongedwa kwanu unsembe, chifukwa kukupatsani mphamvu* kudzatenga masiku 7.+ Levitiko 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Wansembe amene adzadzozedwa+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti atumikire monga wansembe,+ kulowa m’malo+ mwa bambo ake, aziphimba machimo ndipo azivala zovala za nsalu.+ Zovala zimenezo ndi zopatulika.+
29 Zitatero Mose anati: “Dzilimbitseni* lero kuti muchite utumiki kwa Yehova,+ chifukwa aliyense wa inu waukira mwana wake ndi m’bale wake,+ kuti Mulungu akupatseni dalitso lero.”+
33 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kwa masiku 7,+ kufikira tsiku lomaliza la kulongedwa kwanu unsembe, chifukwa kukupatsani mphamvu* kudzatenga masiku 7.+
32 “Wansembe amene adzadzozedwa+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti atumikire monga wansembe,+ kulowa m’malo+ mwa bambo ake, aziphimba machimo ndipo azivala zovala za nsalu.+ Zovala zimenezo ndi zopatulika.+