Deuteronomo 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Uzipereka nsembe ya pasika kwa Yehova Mulungu wako.+ Uzipereka nkhosa ndi ng’ombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+ Deuteronomo 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma uzipereka nsembe ya pasikayo pamalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe kuikapo dzina lake.+ Uzipereka nsembeyo madzulo, dzuwa likangolowa,+ pa nthawi yofanana ndi imene unatuluka mu Iguputo.
2 Uzipereka nsembe ya pasika kwa Yehova Mulungu wako.+ Uzipereka nkhosa ndi ng’ombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+
6 Koma uzipereka nsembe ya pasikayo pamalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe kuikapo dzina lake.+ Uzipereka nsembeyo madzulo, dzuwa likangolowa,+ pa nthawi yofanana ndi imene unatuluka mu Iguputo.