Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 23:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ana aamuna a Amuramu anali Aroni+ ndi Mose.+ Koma Aroni anapatulidwa+ kuti iye ndi ana ake aziyeretsa Malo Oyera Koposa,+ mpaka kalekale. Komanso kuti azifukiza nsembe+ yautsi pamaso pa Yehova, kumutumikira,+ ndi kupereka madalitso+ m’dzina lake mpaka kalekale.

  • 1 Mbiri 26:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa magulu a alonda a pazipatawa, ntchito ya atsogoleri awo inali yofanana ndi ya abale awo,+ ndipo inali yotumikira panyumba ya Yehova.

  • 2 Mbiri 13:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma ife, Yehova ndiye Mulungu wathu+ ndipo sitinamusiye. Ansembe, omwe ndi ana a Aroni, akutumikira Yehova, ndiponso Alevi akugwira ntchito yawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena