Numeri 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lamula ana a Isiraeli kuti, ‘Muzionetsetsa kuti pa nthawi yake yoikidwiratu+ mukupereka kwa ine nsembe yanga, yomwe ndi chakudya changa+ chotentha ndi moto, chotulutsa fungo londikhazika mtima pansi.’+
2 “Lamula ana a Isiraeli kuti, ‘Muzionetsetsa kuti pa nthawi yake yoikidwiratu+ mukupereka kwa ine nsembe yanga, yomwe ndi chakudya changa+ chotentha ndi moto, chotulutsa fungo londikhazika mtima pansi.’+