Deuteronomo 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Limbani mtima ndipo chitani zinthu mwamphamvu.+ Musawaope kapena kuchita nawo mantha,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pang’ono.”+ Yoswa 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ pakuti ndiwe amene utsogolere anthuwa kuti akalandire dziko+ limene ndinalumbirira makolo awo kuti ndidzawapatsa.+ 1 Mbiri 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano taona, Yehova wakusankha kuti umange nyumba yopatulika yoti azikhalamo. Limba mtima ndipo gwira ntchitoyi.”+
6 Limbani mtima ndipo chitani zinthu mwamphamvu.+ Musawaope kapena kuchita nawo mantha,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pang’ono.”+
6 Ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ pakuti ndiwe amene utsogolere anthuwa kuti akalandire dziko+ limene ndinalumbirira makolo awo kuti ndidzawapatsa.+
10 Tsopano taona, Yehova wakusankha kuti umange nyumba yopatulika yoti azikhalamo. Limba mtima ndipo gwira ntchitoyi.”+